Lyrics

Mulungu dalitsani Malawi musunge mtendere Gonjetsani adani, njala, nthenda ndi nsanje, eh Where you from? Malawi! Pakati ku mpoto ku m'mera? Where you from? Malawi! M'makonda komwe n'nabadwila Where you from? Malawi! Pakati ku mpoto ku m'mwera? Where you from? Malawi! M'makonda komwe n'nabadwila Ndimakonda komwe n'nabadwila Zakunja sindisilira Ndine mtumbuka nde ndimanyadira Black girls ndimaiifila Wanyane kweni mulinkhuni, eh? Tikamwe mowa wa nkhuni, eh I am from Malawi phala timamwa la Likuni, eh Ndanyamula mbendera mwina dziko ndikusintha M'mene zinthu zikuyendera Osapusitsika ambuye amatikondela Tinjoye tivine gule wankulu (gule wankulu, gule wankulu) Azimayi kuliza nthungululu (ilililili) Mulungu dalitsani Malawi musunge mtendere Gonjetsani adani, njala, nthenda ndi nsanje, eh Where you from? Malawi! Pakati ku mpoto ku mmwela? Where you from? Malawi! M'makonda komwe n'nabadwila Where you from? Malawi! Pakati ku mpoto ku m'mwera? Where you from? Malawi! (Yeah) M'makonda komwe n'nabadwila Chariz! Dziko la mkaka ndi uchi Kwabata, sungamve mifuti Timapephera nkachisi komaso mzikiti Timalima chamba timalima tea Tiyendereni dindani passport Panga zotheka utenge permit Mukhala mwalandilidwa ndekuti, ayy Timamwa Malawi Gin Ice kuika mchitini Lake Malawi too clean Nsomba nasiya kudya za nchitini Timadya Chambo, Micheni Alenje anyamula mipeni Dzanja linalo chishango Kumbuyo kuli mikondo Mulungu dalitsani Malawi musunge mtendere Gonjetsani adani, njala, nthenda ndi nsanje, eh Where you from? Malawi! Pakati ku mpoto ku m'mera? Where you from? Malawi! M'makonda komwe n'nabadwira Where you from? Malawi! Pakati ku mpoto ku m'mwera? Where you from? Malawi! M'makonda komwe nabadwira
Lyrics powered by www.musixmatch.com
instagramSharePathic_arrow_out