Credits

KOMPOSITION UND LIEDTEXT
Eli Njuchi
Eli Njuchi
Songwriter:in

Lyrics

Pamenepodi, tayetsetsani (pakasuntha) Sispence on the board Njuchi Ngati bundle ndilibe Macheza kulibe Magetsi akathima Macheza kulibe Akati asandiyankhe phone Pa whatsapp blue tick wa ngozi Ndilochepa vutoli lisakule Imva ma solution Bus imodzi ndi ma ola folo Dzina ndi Eli Njuchi nyimbo ikhale follow Ndakwera mu Axa, waku Kaya Ndili mu sienta, waku Lilongwe Shalooomi, Shalo ndikamakatsika makatsika ukanthamangire Shalooomi, Shalo ndikamakatsika makatsika ukanthamangire Long distance loving (Oh oh yeah) Distance loving (Oh oh yeah) Ndigona mu Axa, waku Kaya Long distance loving (Oh oh yeah) Distance loving (Oh oh yeah) Ndili mu sienta waku Lilongwe Pa Lilongwe pompa, ndatopa ndi vamalavu vapa phone Miyendo, nsana, khosi likuwawa Am still coming, I love you, you won't stop me Ndatopa ndi vamalavu vapa phone Tikakumana pa ma tank Shalom Pano pa playlist panga pali Lawi Am gonna walk you home paja kwa Biwi Solution ndi bus imodzi ndi ma ola folo Dzina ndi Eli Njuchi nyimbo ikhale follow Ndakwera mu Axa, waku Kaya Ndili mu sienta, waku Lilongwe Shalooomi, Shalo ndikamakatsika makatsika ukanthamangire Shalooomi, Shalo ndikamakatsika makatsika ukanthamangire Long distance loving (Oh oh yeah) Distance loving (Oh oh yeah) Ndigona mu Axa, waku Kaya Long distance loving (Oh oh yeah) Distance loving (Oh oh yeah) Ndili mu sienta waku Lilongwe Akafunsa za distance bond mufika nazo pati Ayankhe love yathu sangaiyeze ndi mtunda Ndigona mu Axa, waku Kaya Ndili mu sienta, waku Lilongwe Shalooomi, Shalo ndikamakatsika makatsika ukanthamangire Shalooomi, Shalo ndikamakatsika makatsika ukanthamangire Long distance loving (Oh oh yeah) Distance loving (Oh oh yeah) Ndigona mu Axa, waku Kaya Long distance loving (Oh oh yeah) Distance loving (Oh oh yeah) Ndili mu sienta waku Lilongwe Ooh yeah Shalom, Shalom, Shalom
Lyrics powered by www.musixmatch.com
instagramSharePathic_arrow_out