Lyrics

Uh-huh Uh-huh Uh-huh uh-huh uh-huh Tsono Nzawinner Okay Praise the Lord Nduwoneka bho ndavala pantaloné (Uh-huh) Met my ex akuti "Mmh you've changed a lot" The grind don't stop 'till you see the Benz on the parking lot I had no where to go, big bro didn't like my smokin' habits (habits) Pano blessings ndi nyanja ngati ndimagona mkachasi (mkachasi) Hit me up pa den uli ndi ufulu wofukisa tchalisi (tchalisi) Koma fwaka ndi panja fukwa mkati muno nalesa Utha kulinka ndi Eli Njuchi ngati ufuna malesa (malesa) Anthu ena amatha kusintha city utawatenga ku Dedza (ku Dedza) Koma usazafooke uzizapusha uzabooleza (uzabooleza) Ngati siwe Jah Jah uli panja sindupembedza (sindupembedza) Pamalo timatenthetsa (timatenthetsa), matako amagwedeza So many fishes in the sea, Koma uziwa dollar ndi mbeta (mbeta) I wanna get back to my roots kuti azandiyike mu Geneza (Geneza) Ife timafilidwa ndi ana chifukwa timabhebhetsa (timabhebhetsa) Sizachisinsi tiku chaser milli (mili mili) Tikayipeza kuyipanga yambirimbiri (mbiri mbiri) Numbers goin' crazy ndati muyimbire Phini Tizaflipe milli tinapanga mili (mili mili) Mhu Mhu Tinapanga mbiri (mbiri mbiri) Praise the Lord Nduwoneka bho ndavala pantaloné Met my ex akuti "Mmh you've changed a lot" The grind don't stop 'till you see the Benz on the parking lot Fresh out the Trap ndili- Fresh out the Trap ndili drunk and high Highschool kid ndatopa ndikudya ma pie DM sindiyankha hie Don't wonder why most people who do that Amapanga waste my time Mkazi wako amafuna azindikhalira pama thighs Ndakakisser kati ndikumveka gin kalindi breathalyzer Kakuti "Bwanji sumapanga condomize?" Ndati "ndinapanga circumcise" Ndati "ndinapanga circumcise" Ndati "ndinapanga circumcise" Ndati "ndinapanga circumcise" Ndati "ndinapanga circumcise" Ndati "ndinapanga circu" ah
Writer(s): Chifundo Chingaipe Lyrics powered by www.musixmatch.com
instagramSharePathic_arrow_out