Top Songs By Trappybeats.
Similar Songs
Credits
KOMPOSITION UND LIEDTEXT
Ian Derrick Ngalande
Songwriter:in
Lyrics
(Aseh Trappy!)
Eh!
Eh!
Eh! eh!
Internationally ting say
Eh!
Tifela weekend (aah aye)
Tifela weekend (aah aye)
Tifela weekend (aah aye)
Tifela weekend (aah aye)
Motily Moti
Tifela Weekend musabalalike
Lerolo bayala alire
Asanafike adabwitsike payende mowa ngati mtsinje
Tifela Weekend musabalalike
Lerolo bayala alire
Asanafike adabwitsike payende mowa ngati mtsinje
Wabwera wekha ndabwera ndekha ndekha
Iwe tadekha umbombo taleka leka
Wabwera wekha ndabwera ndekha ndekha
Iwe tadekha umbombo taleka leka
Adekhe (Masese)
Adekhe (Masese)
Adekhe (Masese)
Adekhe (Masese)
Eh! Eh! (Adekhe) (Masese)
Adekhe (Masese)
Adekhe (Masese)
Eh! Adekhe (Masese)
Adekhe (Masese)
Adekhe (Masese)
Tifela weekend (adekhe masese)
Tifela weekend (aah aye) Adekhe (Masese)
Tifela weekend (adekhe masese)
Tifela weekend (aah aye) (adekhe) (masese)
Dziko lonse kwakoma ndikuno
Dziko lonse pakoma ndipano
Fada wa Vunga Plan ayy
Lero Tiichemesadi ayy
Aliyense Azipanga zake
Maluziwo usandipake
Wabwera wekha ndabwera ndekha ndekha
Iwe tadekha umbombo taleka leka
Wabwera wekha ndabwera ndekha ndekha
Iwe tadekha umbombo taleka leka
Adekhe (Masese)
Adekhe (Masese)
Adekhe (Masese)
Adekhe (Masese)
Eh! Eh! (Adekhe) (Masese)
Adekhe (Masese)
Adekhe (Masese)
Eh! Adekhe (Masese)
Adekhe (Masese)
Adekhe (Masese)
Tifela weekend (adekhe masese)
Tifela weekend (aah aye) Adekhe (Masese)
Tifela weekend (adekhe masese)
Tifela weekend (aah aye) (adekhe) (masese)
Writer(s): Ian Derrick Ngalande
Lyrics powered by www.musixmatch.com