Top Songs By Eli Njuchi
Similar Songs
Credits
AUSFÜHRENDE KÜNSTLER:INNEN
Eli Njuchi
Künstler:in
KOMPOSITION UND LIEDTEXT
Eli Njuchi
Songwriter:in
Lyrics
Pamtima panga panadza lumpha ndikamva walowa mumpanda,
Walowa munyimba ndimunthu wanga uyu
inde ndi banja komanso munthuyu ndimzanga (munthuyu ndimzanga)
Pali iyeyo kuseka tsiku shota ngati pali iyeyo (pali iyeyo)
pali iyeyo ndimadzidabwa ndekha ngati pali iyeyo mwa ifeyo
Muli mijedu mijedu ndife chi bank cha nkhani
Mijedu mijedu ndife chi bank cha tinkhani muli mijedu
Mije
Mije(kuseka tsiku shota ngati pali iyeyo) mije(pali iyeyo)
Tilindi kujeda a neighbor ndi anzawo tinawaseka
Tilindi kujeda tizibwenzi ta anzake tasekedwa
Nde tikamaseka mpaka misonzi m'masomu
Nde tikamaseka mpaka nthiti kuwawa
Pali iyeyo kuseka tsiku shota ngati pali iyeyo (pali iyeyo)
Pali iyeyo ndimadzidabwa ndekha ngati pali iyeyo
Mwa ifeyo muli mijedu mijedu ndife chi bank cha khani
Mijedu mijedu ndife chi bank cha tinkhani
Mijedu
Lyrics powered by www.musixmatch.com