Credits

KOMPOSITION UND LIEDTEXT
Leumas
Leumas
Songwriter:in
Robert Ching’amba
Songwriter:in
Paul Yankho Chisiano
Paul Yankho Chisiano
Songwriter:in
Tunosiwe Mwakalinga
Tunosiwe Mwakalinga
Songwriter:in
Anthony Malisawa
Anthony Malisawa
Songwriter:in

Lyrics

Mmmh hmm hmm hmm Set up, set up (Eyo tiyeni) (Tiyeni tiyeni tiyeni) (Eish sha sha) Wakutuma ndani Ungandiuze chani Wakutuma ndani Ungandiuze chani Munthu wopanda plan Wochulukitsa nkhani Ungandiuze chani Ungandiuze chani Wakutuma ndani Ungandiuze chani Wakutuma ndani Ungandiuze chani Munthu wopanda plan Wochulukitsa nkhani Ungandiuze chani Ungandiuze chani Chule chule Iwe bwantasa wakutuma ndani Bwantasa kuti ubekeshule Bwantasa mwana wachipongwe Chule chule Iwe bwantasa wakutuma ndani Bwantasa kuti ubekeshule, (uuh) Bwantasa mwana wachipongwe Ndakula movutika Man dekhani Mukachulukitsa nkhani Ife tingoku wekani Ndakula movutika Man dekhani Mukachulukitsa nkhani Ife tingoku wekani Wachibanda ndani Zakulembani Akufuna plan ndani, usachulutse nkhani Uli ndizinga? Uka blaka tisenza Ibweleso ina round Mpakana titentha Koma iwe iwe Iweso nde ndani Kodi wasonkha? Kutizembelera pompa Usamayese iwe iwe iwe Iweso nde ndani? (wakutuma ndani) Kodi wasonkha? Kutizembelera pompa Usamayese iwe Ndakula movutika Man dekhani Mukachulukitsa nkhani Ife tingoku wekani Ndakula movutika Man dekhani Mukachulukitsa nkhani Ife tingoku wekani Chule chule Iwe bwantasa wakutuma ndani Bwantasa kuti ubekeshule Bwantasa mwana wachipongwe Chule chule Iwe bwantasa wakutuma ndani Bwantasa kuti ubekeshule Bwantasa mwana wachipongwe Aaah uh Aaah uh
Lyrics powered by www.musixmatch.com
instagramSharePathic_arrow_out