Similar Songs
Credits
AUSFÜHRENDE KÜNSTLER:INNEN
Tremour
Künstler:in
KOMPOSITION UND LIEDTEXT
Tremour
Komponist:in
Lyrics
Mvera again, again!
One genius tune
100% I prove pa ine sanataye nthawi
Anati ndimulenge mchifanizo changa ndimtere
I'm made of glory and greatness
Moyo wanga anawubebetsa
Too many, many decorations
Complexion tayi cheaker
Plenty plus decorations
Cool lifestyle tayi cheaker
Too many, many decorations
Fanizo la Namalenga
Ayi ooh, pathupi pangapa palibe foul
Really exactly momwe linachokera kwawo
Chabwino chilema chinachita kudza
Kunalembedwa sikuti n'nafuna
Ndipo aliyense ndondomeko ili m'malo (shee)
Zili nde nde nde mawulemele-
Khalidwe la khethekhethe (oh yah)
Umunthu wanga anawubebetsa
100% I prove pa ine sanataye nthawi
Anati ndimulenge mchifanizo changa ndimtere
I'm made of glory and greatness
Moyo wanga anawubebetsa
Too many, many decorations
Complexion tayi cheaker
Plenty plus decorations
Cool lifestyle tayi cheaker
Too many, many decorations
Fanizo la Namalenga
Kalondolondo wati everything is in control
There's no mistake on me at all (oh yeah)
Zili bhobho, he is the God of all the man
Pa ine panatengapo nthawi
Sanangondiwumba opanda plan
Zili nde-nde-nde mawulemele-
Khalidwe la khethekhethe (oh yah)
Umunthu wanga anawubebetsa
100% I prove pa ine sanataye nthawi
Anati ndimulenge mchifanizo changa ndimtere
I'm made of glory and greatness
Moyo wanga anawubebetsa
Too many, many decorations
Complexion tayi cheaker
Plenty plus decorations
Cool lifestyle tayi cheaker
Too many, many decorations
Fanizo la Namalenga
Smile utayi cheaker (hehehehe)
Dimple tayi cheaker
Iwe barber ika seda
Ine ndi fanizo la Namalenga
Wa nsanje idzimcheka
Oh yes I do, yes I
Pa ineyo sanataye nthawi (yeah)
Anati ndimulenge mchifanizo changa ndimtere
I'm made of glory and greatness
Complexion tayi cheaker
Plenty plus decorations
Cool lifestyle right yeah da
Too many, many decorations
Fanizo la Namalenga
Looks tayi cheaker
Fanizo la Namalenga (ooh!)
Oooh
Lyrics powered by www.musixmatch.com