Top Songs By Crispy Malawi
Credits
AUSFÜHRENDE KÜNSTLER:INNEN
Crispy Malawi
Künstler:in
KOMPOSITION UND LIEDTEXT
Chifundo Chingaipe
Komponist:in
PRODUKTION UND TECHNIK
Steve Chriss
Produzent:in
FAMOUS
Mischtechniker:in
Lyrics
Mhaaahahahaha
Malawian
Yeah
265 (fuck it bro)
Spe
Sound Gawwd
Ena aku shophetsa Ganja (Ganja)
Ena aku shophetsa Fanta (Fanta)
Ena amagulitsa mpasha kukana kumwa ice London (Ice London)
Bola gin ndi fwaka (fwaka)
Nde uzikonda Ku husser (hustle)
Legal or illegal Boma silingakupatse Mpamba mphwanga
A police ndi Abale Athu
Apolice ndi Abale Athu
Apolice ndi Abale Athu
Apolice (Apolice) ndi Abale Athu
Kupeza Money ndi (ushasha)
Ndine street smart (Hustler)
With my Self Made (kwacha)
Blessings kuno ndiku (Mtaja )
Kupeza Money ndi (ushasha)
Ndine street smart (Hustler)
With my Self Made (kwacha)
Blessings kuno ndiku (Mtaja)
40pin kuipanga ikhale 80pin
Sizikufunika Degree
Ndiza Straight can’t you See?
Ungoika Focus
Umve zomwe ndikunenazi
Anthu ndi Ama Jelousy
Uka ma Chaser zi paper zi
Rule number one
Be yourself don't try to be me
Uka Burner ka Cannabis
Kosala uzikabisa
Be Your Plug
Cut off your Middle man
Ma Move amadhulisa
Basi maluzi taakhaulitsa
Ena aku shophetsa Ganja (Ganja)
Ena aku shophetsa Fanta (Fanta)
Ena amagulitsa mpasha kukana kumwa ice London (London)
Bola gin ndi fwaka (fwaka)
Nde uzikonda Ku husser (hustle)
Legal or illegal Boma silingakupatse Mpamba(ha ha) mphwanga (ha)
Apolice ndi Abale Athu (Athu)
Apolice (Apolice) ndi Abale Athu (ndi abale athu)
Apolice ndi A Bale Athu (ndi abale athu)
Apolice (Apolice) ndi Abale Athu
Kupeza Money ndi (ushasha)
Ndine street smart (Hustler)
With my Self Made (kwacha)
Blessings kuno ndiku (Mtaja )
Kupeza Money ndi (ushasha)
Ndine street smart (Hustler)
With my Self Made (kwacha)
Blessings kuno ndiku (Mtaja)
Kukonda ku woker figure ku Hita G spot (G spot)
Hustle imayamba aka hitta record (record)
Iiih Ukufuna Beef ase eko T bone
Ndafika ndi stainado Wachika ku CICOD
Spe ndi King of The ghetto fredo ndi ghetto king kong
Funa kupanga Billi kuvutisa ku ding dong
Nyimbo zolemba ku ma Message pano ndima Ringtone
Ma Verse angozaza funa ndipeze Vepi ku Synod
Gist yako ipeze vep ine Ndilibe Nayo ntchito(ntchito)
She’s in my bed after iwe kumutengera Galitos
Uma Trappa ndima Chick koma onunkha zitosi (shit)
Ndili mmutu mwama Diva ngati ribbon
Ndangotulusa Chida weapon
Ena aku shophetsa Ganja (Ganja)
Ena aku shophetsa Fanta (Fanta)
Ena amagulitsa mpasha kukana kumwa ice London (Ice London)
Bola gin ndi fwaka (fwaka)
Nde uzikonda Ku husser (hustle)
Legal or illegal Boma silingakupatse Mpamba mphwanga
Apolice (Apolice) ndi Abale Athu (ndi abale athu)
Apolice (Apolice) ndi Abale Athu
Apolice (Apolice) ndi Abale Athu (ndi abale athu)
Apolice ndi A Bale Athu
Kupeza Money ndi (ushasha)
Ndine street smart (Hustler)
With my Self Made (kwacha)
Blessings kuno ndiku (Mtaja )
Kupeza Money ndi (ushasha)
Ndine street smart (Hustler)
With my Self Made (kwacha)
Blessings kuno ndiku (Mtaja)
Mtaja
Mtaja
Kodi wagoma kapena wapeza Ku mtaja
Mtaja
Mtaja
Nditha Ku doja
Written by: Chifundo Chingaipe