Top Songs By EvanzMuzik
Similar Songs
Credits
KOMPOSITION UND LIEDTEXT
Evans Chimwala
Songwriter:in
Lyrics
Ndinamva zoti unali ndi chinkhoswe
Ayi congrats zabwino zonse
Anthu mukukula enafe tingokula mtima
Ine ndizakwatila ndikazagula Bima
Save the date ine ndikusaver money
Muka boys quarter rent sifika 100
Akafunsa tivina liti moyelekedwa
Ndimayankha, ndidzakwatila koma mochedwa
I hope zikuyenda ndimangoti ndikuhale
I know papita nthawi komabe singayiwale
Tili pa chibwezi tili ana kalekale
Ndinalibe Dollar, Mphasha kapena njale
Koma machezedwe athu kumvetsetsana kwathu
Pamene zinafika nkanakadinditsa tattoo
Pena ndimangoima mu shower kuganizila
Zoti pano chinatha ngati akutinamizila
Aaaah sindingayiwale za iwe
Aaaah sindingayiwale za iwe
Sindinkafuna ndizifunsa ulikuti
Nsanje inkandipangitsa kufuna kugula mfuti
Ngati body guard wako daily ndinali pa duty
Plan yathu inali yosavala Vero ndi Suit
Koma ndithu sindimvetsa ndimayesa sizitheka
Unatenga mtima wanga osasiya olo theka
Nkhope yako ngati yapa account ya Fake
Ex unali ansa ngati Jane MEC
Ndimablema maluzi ankandichotssa Confi
Plus kavalidwe inali ngozi
Ndimayang'ana pansi tikamayenda limodzi
Pena ndimapereka ma excuse
Ndili mu elaz pano ndinapeza vephi
Zinthu zikayenda mwina ndipeza bebi
Koma pena ndimangoyima mu shower kuganizila
Zoti pano chinatha ngati akutinamizila
Sindingayiwale, za iwe
I can never forget, about you
No no no no
Aah Sindingayiwale
Written by: Evans Chimwala