Lyrics

My, my name is EvanzMuzik And I'm uh, a hip hop story teller Listen Chaka chino ndungofuna kusintha mindset yanga Ambiri ndiwatuluka ndisintha number yanga Ndufuna ndidzipatse chinthawi chodzitolera Pali zinthu zingapo ndimafuna nditagela Chaka chino ndufuna ndiphuzire kudziletsa Ndidzingowapewa anthu ofuna kundiyesa Ndiphunzire kufuna kudziwa, mkudzichepetsa Ndiphunzire kulimbikira osati macheza Ndikufuna ndiphunzire kumangopanga zanga Ndiphunzire kukana kukamba nkhani yoti siyanga Ndiphunzire kutsogoza Mulungu pa chilichonse ndikupanga Ndikufuna kuphunzira kumakhululuka nsanga Makamaka ndikufuna ndiphuzire kupemphera Ndiphuzire kupitiliza pomwe ndikulephera Ndiphunzire, kusunga zinsinsi pa society Ndiphunzire zambiri za servitude ndi loyalty Ndikufuna Ndiphunzire kukhala sober Ndiphunzire kupilira akazanditchula zoba Topic ya zachikondi chonde gaireni notes Ndukufuna Ndiphunzire kukhala ndi mkazi m'modzi Ndiphunzitseni, ndiphunzitseni Ndiphunzitseni, ndiphunzitseni Ndiphunzitseni, ndiphunzitseni Ndiphunzitseni, ndiphunzitseni Ndiphunzitseni, ndiphunzitseni
Lyrics powered by www.musixmatch.com
instagramSharePathic_arrow_out