Top Songs By Baxxy Mw
Credits
KOMPOSITION UND LIEDTEXT
Happy Titani Bakolo
Songwriter:in
Madalitso Kamtema
Songwriter:in
Mike Mkhaya
Songwriter:in
Lyrics
(Ayo Billy!)
Ouh ouh ouh ouh ouh, yeah
Poti Mulungu samakhala kwanu
Mdalitso wanga sungakhale wanu
Osandipana pana pana ngati nkhanu
Chonde muzipanga zanu
But we getting blessed every day
Zima blessings mbwe mbwe mbwe
But we getting blessed every day
Zima blessings mbwe mbwe mbwe
Tikungomveka muzima speaker
Tili pa Radio, Zimachitika
God been cooking, ali kum'phika
KungoSonyeza, ma blessings angotsika
Problems getting smaller, 'cause we getting bigger
Ndikumadhula ku show, ndumacharger mita
Kuthoka facts osakubisila
Ndikuma praisa aise Paulo ndi Silla
Zandipana zima blessings
I'm no longer stressing
It might look so tempting
Tell that shit to rest in peace
Poti Mulungu samakhala kwanu
Mdalitso wanga sungakhale wanu
Osandipana pana pana ngati nkhanu
Chonde muzipanga zanu
But we getting blessed every day
Zima blessings mbwe mbwe mbwe
But we getting blessed every day
Zima blessings mbwe mbwe mbwe
Ndimatha kuvala sinditha ndewu
Zama show nnakwera mtengo Zakeyu
Nthawi yanga inangokwana nnaliza belu
Yeah I've been trynna get the money, shut up let me tell you
Hakuna Matata! Almighty Father
You made me a dada
Imma touch more dollars
Iyi si Pasada ife tima trapper
Mfana ozitsata, amandiyada
I'm from the ghetto yeah, ndaona zokhoma
koma timalimbikira mpaka kumveka mma boma
Ambuye amandikonda eya zoona,
ndachimwa kwambiri kwangotsala ndikuborna
Poti Mulungu samakhala kwanu
Mdalitso wanga sungakhale wanu
Osandipana pana pana ngati nkhanu
Chonde muzipanga zanu
But we getting blessed every day
Zima blessings mbwe mbwe mbwe
But we getting blessed every day
Zima blessings mbwe mbwe mbwe
Yo
game kudabwa afika liti madhala
Paja ana a mulungu kufika ngati mbala
Mkati, ndikumveka kutsutsa
Koma nkayimba nawo akuwusa
Vuto nkayimba ndekha ndi suicide
Koma nkapanga dollar akufunsa
Life yanga ndi movie, n'kati ndifile ngati Rambo
Ndi Princess pa den afuna tichille ngati jungle
Ma rapper akufuna andi-yuze, nah I'm too hard to handle
Mfana oyaka, mfana oyabwa ngati fungal
Poti Mulungu samakhala kwanu
Mdalitso wanga sungakhale wanu
Osandipana pana pana ngati nkhanu
Chonde muzipanga zanu
But we getting blessed every day
Zima blessings mbwe mbwe mbwe
But we getting blessed every day
Zima blessings mbwe mbwe mbwe
Lyrics powered by www.musixmatch.com