Letras

Classroom
Step in the class with j4 kuphadzi
Milomo ili bi ngati ndimadya zi blust
Diso lili pyu eya ndina khota kwa rasi
All eyes on me when I enter in the class
Madam kundisaka ngati dick
Register ungojomba mpaka week
Fees samangotola ngati pic ( photo )
Muzivele chisoni mukakhala please
In the class pachi corner
Ngati weed ma baby angolora
Sala mulibe ndachikhola chi frola
Kuyendesa mouse mpaka kukafika ku ova
In the class ndichi bestie busy kulowa ma beat zapa desk
Ndimajomba kukhala kuli test
Bag mwa mwana wa school mupedzeka bwanji toti
In the class amangoti ndine gothi
Dollar yama kope nagulira Vlone
Ngati L-City kugeli ndikawale
Kugeli kusitha kicks call me palanawe
Pota kako name break tikalawe
In the class desho wanga ndi jac
Alibe nzeru koma ali ndichi nyash
Anandikana ati ndingokhala son
Ndiwowala kuwala kuposa sun
In the class play with Rabia majola
Kuphadzi airforce koma ntchito yosachonga
Msonkhano wamakolo dala sindimaikocha
Very good very good si phyzo kope mulibe good
In the class ndimadada kupota ndudu
In the class ku dripper ndikachaso
Ngati ndimamwa jada
In the class
In the class
In the class
Drip in the class
In the class
Written by: SKHRIZY, Unique Musiq
instagramSharePathic_arrow_out