Top Songs By Gwamba
Credits
AUSFÜHRENDE KÜNSTLER:INNEN
Gwamba
Künstler:in
KOMPOSITION UND LIEDTEXT
Gwamba
Songwriter:in
PRODUKTION UND TECHNIK
Henwood
Produzent:in
BFB
Produzent:in
Tricky Beats
Produzent:in
Lyrics
Yo, ndili mfana nimkafuna nditagwira ka dollar
Pano ndukapeza koma kusowa wo caller
Kuyang'anana mu phone mwangamu mwadzadza mbola
Mafuso achuluka koma oyankha akusowa
Questions, kodi ndimalakwitsa chani?
Anali anzanga pano asanduka adani
Pena ndumafila ngati Mbuye is tryna try me
Mwina andikokeko coz I feel like I'm drowning
Questions, kodi mufuna mpange choose?
Pakati pa azinzanga mkukhala maluzi?
Ena andinena nde mtima ukuwawadi
N'nasankha greener pasture nde sindimalowa blues
Kale ngini imashupha, eh
Koma Yesu ananditsuka, ey
Iye samandiweluza, no
Nkona lero akundi user, mmh
Anzako amakunena chakutali, ey
Anzako amakunena chakumbali, oh
Anzako amakunena chakutali, ey
Anzako amakunena chakumbali, oh
Uzampeza wina (uzampeza)
Ndinampeza wina (ndinampeza)
Uzampeza wina (uzampeza)
Ndinampeza wina (ndinampeza)
Ey, tinkati tsiku lina nafe tidzakhalako adad)
Tizachoka kuma ghetto kushala ku ma yard
Tizamenya ma collabo m'mafana akunja
Ndipo Mulungu akalora tizayamba ma award
Mesa unali nzanga pano ndiwe hater
Ufuna ndipepese poti ngini ikuyenda
Nsanje ndi matenda
Nde mtima ukumandiwawa poti unandisiya ndekha ndizi ma pretender
Mwina ndipepese ngini yoti Ine sin'nalakwe
Now I keep it real zikumuwawayo zake
Love everybody, word from my mama
Ine chiponge sindibweza m'madalira khama
Kale ngini imashupha, eh
Koma Yesu ananditsuka, ey
Iye samandiweluza, no
Nkona lero akundi user, mmh
Anzako amakunena chakutali, ey
Anzako amakunena chakumbali, oh
Anzako amakunena chakutali, ey
Anzako amakunena chakumbali, oh
Uzampeza wina (uzampeza)
Ndinampeza wina (ndinampeza)
Uzampeza wina (uzampeza)
Ndinampeza wina
Anzako amakunena chakutali, ey
Anzako amakunena chakumbali, oh
Anzako amakunena chakutali, ey
Anzako amakunena chakumbali, oh
Uzampeza wina (uzampeza)
Ndinampeza wina (ndinampeza)
Uzampeza wina (uzampeza)
Ndinampeza wina
Written by: Duncan Gwamba Zgambo